Numeri 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye anawauza kuti: “Mvetserani mawu anga. Pakanakhala mneneri wa Yehova pakati panu, ndikanamudziwitsa za ine mʼmasomphenya,+ ndipo ndikanalankhula naye mʼmaloto.+
6 Iye anawauza kuti: “Mvetserani mawu anga. Pakanakhala mneneri wa Yehova pakati panu, ndikanamudziwitsa za ine mʼmasomphenya,+ ndipo ndikanalankhula naye mʼmaloto.+