Salimo 43:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tumizani kuwala kwanu ndi choonadi chanu.+Zimenezi zinditsogolere.+Zindifikitse kuphiri lanu lopatulika ndi kuchihema chanu chachikulu.+ Salimo 47:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti Yehova, Wam’mwambamwamba, ndi wochititsa mantha,+Ndiye Mfumu yaikulu padziko lonse lapansi.+ Salimo 66:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Bwerani anthu inu, kuti muone ntchito za Mulungu.+Zimene wachitira ana a anthu ndi zochititsa mantha.+ Salimo 73:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kufikira pamene ndinalowa m’malo opatulika aulemerero a Mulungu.+Ndinafuna kudziwa za tsogolo lawo.+
3 Tumizani kuwala kwanu ndi choonadi chanu.+Zimenezi zinditsogolere.+Zindifikitse kuphiri lanu lopatulika ndi kuchihema chanu chachikulu.+
2 Pakuti Yehova, Wam’mwambamwamba, ndi wochititsa mantha,+Ndiye Mfumu yaikulu padziko lonse lapansi.+
5 Bwerani anthu inu, kuti muone ntchito za Mulungu.+Zimene wachitira ana a anthu ndi zochititsa mantha.+
17 Kufikira pamene ndinalowa m’malo opatulika aulemerero a Mulungu.+Ndinafuna kudziwa za tsogolo lawo.+