Salimo 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu Yehova, nditsogolereni m’chilungamo chanu+ chifukwa adani anga andizungulira.+Salazani njira yanu kuti ndiyendemo popanda chopunthwitsa.+ Salimo 27:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndilangizeni, inu Yehova, kuti ndiyende m’njira yanu.+Nditsogolereni m’njira yowongoka kuti nditetezeke kwa adani anga. Salimo 143:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiphunzitseni kuchita chifuniro chanu,+Pakuti inu ndinu Mulungu wanga.+Mzimu wanu ndi wabwino.+Unditsogolere m’dziko la olungama.+
8 Inu Yehova, nditsogolereni m’chilungamo chanu+ chifukwa adani anga andizungulira.+Salazani njira yanu kuti ndiyendemo popanda chopunthwitsa.+
11 Ndilangizeni, inu Yehova, kuti ndiyende m’njira yanu.+Nditsogolereni m’njira yowongoka kuti nditetezeke kwa adani anga.
10 Ndiphunzitseni kuchita chifuniro chanu,+Pakuti inu ndinu Mulungu wanga.+Mzimu wanu ndi wabwino.+Unditsogolere m’dziko la olungama.+