Nehemiya 9:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Munawapatsa mzimu wanu wabwino+ kuti akhale anzeru. Simunawamane mana+ ndipo munawapatsa madzi kuti athetse ludzu lawo.+ Yohane 14:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Koma mthandizi, amene ndi mzimu woyera, amene Atate wanga adzatumiza m’dzina langa, adzakuphunzitsani zinthu zonse ndi kukukumbutsani zonse zimene ndinakuuzani.+
20 Munawapatsa mzimu wanu wabwino+ kuti akhale anzeru. Simunawamane mana+ ndipo munawapatsa madzi kuti athetse ludzu lawo.+
26 Koma mthandizi, amene ndi mzimu woyera, amene Atate wanga adzatumiza m’dzina langa, adzakuphunzitsani zinthu zonse ndi kukukumbutsani zonse zimene ndinakuuzani.+