Salimo 23:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Amatsitsimula moyo wanga.+Amanditsogolera m’tinjira tachilungamo chifukwa cha dzina lake.+ Salimo 25:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyendetseni m’choonadi chanu ndi kundiphunzitsa,+Pakuti inu ndinu Mulungu wa chipulumutso changa.+ ו [Waw]Chiyembekezo changa chili mwa inu tsiku lonse.+
5 Ndiyendetseni m’choonadi chanu ndi kundiphunzitsa,+Pakuti inu ndinu Mulungu wa chipulumutso changa.+ ו [Waw]Chiyembekezo changa chili mwa inu tsiku lonse.+