Salimo 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu Yehova, nditsogolereni m’chilungamo chanu+ chifukwa adani anga andizungulira.+Salazani njira yanu kuti ndiyendemo popanda chopunthwitsa.+ Salimo 31:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti inu ndinu thanthwe langa ndi malo anga achitetezo.+Chifukwa cha dzina lanu+ mudzanditsogolera ndi kundilozera njira.+ Miyambo 8:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndimayenda m’njira yachilungamo,+ komanso pakati pamisewu yachilungamo,+
8 Inu Yehova, nditsogolereni m’chilungamo chanu+ chifukwa adani anga andizungulira.+Salazani njira yanu kuti ndiyendemo popanda chopunthwitsa.+
3 Pakuti inu ndinu thanthwe langa ndi malo anga achitetezo.+Chifukwa cha dzina lanu+ mudzanditsogolera ndi kundilozera njira.+