Salimo 72:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Aweruzire anthu milandu mwachilungamo,+Ndipo aweruze milandu ya osautsika ndi ziweruzo zolungama.+ Yesaya 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Adzaweruza mwachilungamo anthu onyozeka+ ndipo adzadzudzula anthu mowongoka mtima, pothandiza ofatsa a padziko lapansi. Adzakwapula dziko lapansi ndi ndodo ya pakamwa pake,+ ndipo adzagwiritsa ntchito mzimu wa pakamwa pake kupha munthu woipa.+ Yesaya 42:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Taonani mtumiki wanga+ amene ndamugwiritsitsa,+ amene ndamusankha,+ ndiponso amene moyo wanga ukukondwera naye.+ Ine ndaika mzimu wanga mwa iye,+ ndipo iye adzabweretsa chilungamo kwa anthu a mitundu ina.+
4 Adzaweruza mwachilungamo anthu onyozeka+ ndipo adzadzudzula anthu mowongoka mtima, pothandiza ofatsa a padziko lapansi. Adzakwapula dziko lapansi ndi ndodo ya pakamwa pake,+ ndipo adzagwiritsa ntchito mzimu wa pakamwa pake kupha munthu woipa.+
42 Taonani mtumiki wanga+ amene ndamugwiritsitsa,+ amene ndamusankha,+ ndiponso amene moyo wanga ukukondwera naye.+ Ine ndaika mzimu wanga mwa iye,+ ndipo iye adzabweretsa chilungamo kwa anthu a mitundu ina.+