Salimo 45:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Umakonda chilungamo+ ndipo umadana ndi zoipa.+N’chifukwa chake Mulungu, Mulungu wako,+ wakudzoza+ ndi mafuta achikondwerero chachikulu+ kuposa cha mafumu ena.+ Miyambo 31:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tsegula pakamwa pako, weruza mwachilungamo ndipo thandiza munthu wosautsika ndi wosauka pa mlandu wake.+
7 Umakonda chilungamo+ ndipo umadana ndi zoipa.+N’chifukwa chake Mulungu, Mulungu wako,+ wakudzoza+ ndi mafuta achikondwerero chachikulu+ kuposa cha mafumu ena.+
9 Tsegula pakamwa pako, weruza mwachilungamo ndipo thandiza munthu wosautsika ndi wosauka pa mlandu wake.+