Salimo 19:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chilamulo+ cha Yehova ndi changwiro,+ chimabwezeretsa moyo.+Zikumbutso+ za Yehova ndi zodalirika,+ zimapatsa nzeru munthu wosadziwa zinthu.+ Salimo 51:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Bwezeretsani mwa ine chisangalalo chifukwa cha chipulumutso chanu,+Ndichirikizeni ndi mzimu wofunitsitsa.+
7 Chilamulo+ cha Yehova ndi changwiro,+ chimabwezeretsa moyo.+Zikumbutso+ za Yehova ndi zodalirika,+ zimapatsa nzeru munthu wosadziwa zinthu.+
12 Bwezeretsani mwa ine chisangalalo chifukwa cha chipulumutso chanu,+Ndichirikizeni ndi mzimu wofunitsitsa.+