Salimo 119:111 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 111 Ndatenga zikumbutso zanu kukhala chuma changa mpaka kalekale,+Pakuti zimakondweretsa mtima wanga.+ Salimo 119:129 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 129 Zikumbutso zanu n’zodabwitsa.+N’chifukwa chake ine ndimazisunga.+ Salimo 132:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ana ako akadzasunga pangano langa+Ndi zikumbutso zanga zimene ndidzawapatsa,+Ngakhalenso ana awo+Adzakhala pampando wako wachifumu kwamuyaya.”+ 2 Petulo 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Okondedwa, iyi tsopano ndi kalata yachiwiri imene ndikukulemberani, ndipo monga yoyamba ija,+ ndikulimbikitsa mphamvu zanu zotha kuganiza bwino mwa kukukumbutsani,+
111 Ndatenga zikumbutso zanu kukhala chuma changa mpaka kalekale,+Pakuti zimakondweretsa mtima wanga.+
12 Ana ako akadzasunga pangano langa+Ndi zikumbutso zanga zimene ndidzawapatsa,+Ngakhalenso ana awo+Adzakhala pampando wako wachifumu kwamuyaya.”+
3 Okondedwa, iyi tsopano ndi kalata yachiwiri imene ndikukulemberani, ndipo monga yoyamba ija,+ ndikulimbikitsa mphamvu zanu zotha kuganiza bwino mwa kukukumbutsani,+