Salimo 25:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 M’njira zonse za Yehova muli kukoma mtima kosatha ndi choonadiKwa anthu osunga pangano+ lake ndi zikumbutso zake.+ Salimo 119:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Odala ndi anthu amene amasunga zikumbutso zake,+Amene amayesetsa kumufunafuna ndi mtima wonse.+
10 M’njira zonse za Yehova muli kukoma mtima kosatha ndi choonadiKwa anthu osunga pangano+ lake ndi zikumbutso zake.+