Salimo 119:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Osangalala ndi anthu amene amasunga zikumbutso zake,+Amene amamufunafuna ndi mtima wawo wonse.+