Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 4:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 “Mukadzafufuza Yehova Mulungu wanu muli kumeneko, mudzam’pezadi,+ chifukwa mudzam’funafuna ndi mtima wanu wonse ndiponso moyo wanu wonse.+

  • 1 Mafumu 8:48
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 48 n’kubwerera kwa inu ndi mtima wawo wonse+ ndi moyo wawo wonse, m’dziko la adani awo amene anawagwira ndiponso akapemphera kwa inu atayang’ana kudziko lawo limene munapatsa makolo awo, kumzinda umene mwasankha ndi nyumba ya dzina lanu imene ndamanga,+

  • 1 Mbiri 22:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Choncho funafunani Yehova Mulungu wanu+ ndi mtima wanu ndi moyo wanu.+ Yambani kumanga nyumba yopatulika+ ya Yehova Mulungu woona.+ Kenako mukatenge likasa+ la pangano la Yehova ndi ziwiya zopatulika za Mulungu woona n’kuziika m’nyumba ya dzina+ la Yehova imene imangidweyo.”

  • 2 Mbiri 31:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Anagwira ndi mtima wake wonse+ ntchito iliyonse imene anaiyamba mu utumiki+ wa panyumba ya Mulungu woona ndi m’chilamulo,+ pofunafuna+ Mulungu wake, ndipo zinthu zinamuyendera bwino.+

  • Yeremiya 29:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 “‘Inu mudzandifunafuna ndipo mudzandipeza+ chifukwa mudzandifunafuna ndi mtima wanu wonse.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena