Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 30:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Adzachita zimenezi popeza udzamvera mawu a Yehova Mulungu wako ndi kusunga malamulo ake ndi mfundo zake zolembedwa m’buku ili la chilamulo,+ chifukwa udzabwerera kwa Yehova Mulungu wako ndi mtima wako wonse ndi moyo wako wonse.+

  • 2 Mbiri 15:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Koma iwo atabwerera kwa Yehova Mulungu wa Isiraeli+ m’mavuto awowo+ n’kumufunafuna, iye analola kuti amupeze.+

  • 2 Mbiri 15:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ayuda onse anayamba kusangalala+ chifukwa cha zimene analumbirazo popeza analumbira ndi mtima wawo wonse, komanso chifukwa chakuti anafunafuna Mulungu mokondwa kwambiri moti iye analola kuti amupeze.+ Choncho Yehova anapitiriza kuwapatsa mpumulo pakati pa adani awo onse owazungulira.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena