Deuteronomo 4:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pamapeto pake, mawu amenewa akadzakwaniritsidwa pa inu, n’kukhala pamavuto aakulu, mudzabwereradi kwa Yehova Mulungu wanu+ ndi kumvetsera mawu ake.+ Salimo 106:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Mulungu akamva kuchonderera kwawo+Anali kuona kuvutika kwawo.+ Aroma 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Aliyense wochita zoipa, kuyambira Myuda+ mpaka Mgiriki,+ adzaona nsautso ndi zowawa.
30 Pamapeto pake, mawu amenewa akadzakwaniritsidwa pa inu, n’kukhala pamavuto aakulu, mudzabwereradi kwa Yehova Mulungu wanu+ ndi kumvetsera mawu ake.+