Salimo 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma onse othawira kwa inu adzakondwa.+Adzafuula mokondwera mpaka kalekale.*+Ndipo inu mudzawateteza.Okonda dzina lanu adzakondwa chifukwa cha inu.+ Salimo 40:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Onse amene akufunafuna inu,+Akondwere ndi kusangalala mwa inu.+Onse amene amakonda chipulumutso chanu,+Nthawi zonse azinena kuti: “Yehova alemekezeke.”+
11 Koma onse othawira kwa inu adzakondwa.+Adzafuula mokondwera mpaka kalekale.*+Ndipo inu mudzawateteza.Okonda dzina lanu adzakondwa chifukwa cha inu.+
16 Onse amene akufunafuna inu,+Akondwere ndi kusangalala mwa inu.+Onse amene amakonda chipulumutso chanu,+Nthawi zonse azinena kuti: “Yehova alemekezeke.”+