Salimo 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chipulumutso chimachokera kwa Yehova.+Madalitso anu ali pa anthu anu.+ [Seʹlah.] Salimo 85:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndithudi, chipulumutso chake chili pafupi ndi amene amamuopa,+Kuti ulemerero ukhale m’dziko lathu.+
9 Ndithudi, chipulumutso chake chili pafupi ndi amene amamuopa,+Kuti ulemerero ukhale m’dziko lathu.+