Salimo 85:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndithudi, iye ndi wokonzeka kupulumutsa amene amamuopa,+Kuti ulemerero wake ukhale mʼdziko lathu.