Salimo 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma ine ndakhulupirira kukoma mtima kwanu kosatha.+Mtima wanga ukondwere chifukwa cha chipulumutso chanu.+ Salimo 68:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma olungama asangalale,+Asekerere pamaso pa Mulungu,+Ndipo akondwere ndi kusangalala.+
5 Koma ine ndakhulupirira kukoma mtima kwanu kosatha.+Mtima wanga ukondwere chifukwa cha chipulumutso chanu.+