1 Samueli 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno Hana anayamba kupemphera+ kuti:“Mtima wanga ukukondwera mwa Yehova,+Nyanga* yanga yakwezekadi kudzera mwa Yehova.+Ndikutsutsana ndi adani anga molimba mtima,Pakuti ndikukondwera ndi chipulumutso chochokera kwa inu.+ Luka 1:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Ndipo mzimu wanga sungaleke kusefukira+ ndi chimwemwe mwa Mulungu, Mpulumutsi wanga.+
2 Ndiyeno Hana anayamba kupemphera+ kuti:“Mtima wanga ukukondwera mwa Yehova,+Nyanga* yanga yakwezekadi kudzera mwa Yehova.+Ndikutsutsana ndi adani anga molimba mtima,Pakuti ndikukondwera ndi chipulumutso chochokera kwa inu.+