Salimo 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndidzaimbira Yehova chifukwa wandifupa ndi zinthu zabwino.+ Luka 1:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Pamenepo Mariya anati: “Moyo wanga ukulemekeza Yehova.+ Aroma 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndipo si zokhazo, koma tikukondweranso mwa Mulungu kudzera mwa Ambuye wathu Yesu Khristu, amene tayanjanitsidwa ndi Mulungu kudzera mwa iye.+
11 Ndipo si zokhazo, koma tikukondweranso mwa Mulungu kudzera mwa Ambuye wathu Yesu Khristu, amene tayanjanitsidwa ndi Mulungu kudzera mwa iye.+