1 Samueli 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno Hana anayamba kupemphera+ kuti:“Mtima wanga ukukondwera mwa Yehova,+Nyanga* yanga yakwezekadi kudzera mwa Yehova.+Ndikutsutsana ndi adani anga molimba mtima,Pakuti ndikukondwera ndi chipulumutso chochokera kwa inu.+ Salimo 34:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndidzadzitamandira mwa Yehova.+Ofatsa adzamva ndi kukondwera.+
2 Ndiyeno Hana anayamba kupemphera+ kuti:“Mtima wanga ukukondwera mwa Yehova,+Nyanga* yanga yakwezekadi kudzera mwa Yehova.+Ndikutsutsana ndi adani anga molimba mtima,Pakuti ndikukondwera ndi chipulumutso chochokera kwa inu.+