Salimo 119:74 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 74 Oopa inu ndi amene amasangalala akandiona,+Chifukwa ndayembekezera mawu anu.+