Salimo 119:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Kuti ndipeze choyankha kwa wonditonza,+Pakuti ine ndakhulupirira mawu anu.+ Salimo 119:147 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 147 Ndadzuka m’mawa kuli mbuu,+ kuti ndipemphe thandizo kwa inu,+Pakuti ndayembekezera mawu anu.+