Salimo 119:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Kumbukirani mawu amene munandiuza ine mtumiki wanu,+Mawu amene ndikuwayembekezera malinga ndi lonjezo lanu.+ Salimo 119:81 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 81 Ine ndafooka chifukwa cholakalaka chipulumutso chanu,+Pakuti ndayembekezera mawu anu.+ Salimo 119:105 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 105 Mawu anu ndi nyale younikira kumapazi anga,+Ndi kuwala kounikira njira yanga.+
49 Kumbukirani mawu amene munandiuza ine mtumiki wanu,+Mawu amene ndikuwayembekezera malinga ndi lonjezo lanu.+