Salimo 119:74 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 74 Oopa inu ndi amene amasangalala akandiona,+Chifukwa ndayembekezera mawu anu.+ Salimo 119:114 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 114 Inu ndinu malo anga obisalamo ndi chishango changa,+Pakuti ndayembekezera mawu anu.+