Salimo 119:74 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 74 Amene amakuopani amasangalala akandiona,Chifukwa mawu anu ndi chiyembekezo changa.*+