2 Samueli 7:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Tsopano inu Yehova Mulungu, chitani mpaka kalekale mawu amene mwalankhula okhudza mtumiki wanu ndi nyumba yake. Chitani mmene mwanenera.+ Salimo 105:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Iye anakumbukira lonjezo lake loyera limene analonjeza mtumiki wake Abulahamu.+ Salimo 106:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Zikatero anali kukumbukira pangano limene anachita ndi iwo,+Ndipo anali kuwamvera chisoni chifukwa cha kuchuluka kwa kukoma mtima kwake kosatha.+
25 “Tsopano inu Yehova Mulungu, chitani mpaka kalekale mawu amene mwalankhula okhudza mtumiki wanu ndi nyumba yake. Chitani mmene mwanenera.+
45 Zikatero anali kukumbukira pangano limene anachita ndi iwo,+Ndipo anali kuwamvera chisoni chifukwa cha kuchuluka kwa kukoma mtima kwake kosatha.+