-
1 Mbiri 17:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Tsopano inu Yehova, mawu amene mwalankhula okhudza mtumiki wanu ndi nyumba yake, akhale oona mpaka kalekale, ndipo chitani mmene mwanenera.
-