Salimo 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inu Yehova, m’mawa mudzamva mawu anga,+M’mawa ndidzalankhula nanu ndipo ndidzadikira yankho.+ Salimo 88:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma ine ndafuulira inu Yehova kupempha thandizo,+Ndipo m’mawa mapemphero anga amafika kwa inu nthawi zonse.+ Maliko 1:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 M’mawa kwambiri kukali mdima, Yesu anadzuka ndi kutuluka panja, ndipo anapita kumalo kopanda anthu.+ Kumeneko anayamba kupemphera.+
13 Koma ine ndafuulira inu Yehova kupempha thandizo,+Ndipo m’mawa mapemphero anga amafika kwa inu nthawi zonse.+
35 M’mawa kwambiri kukali mdima, Yesu anadzuka ndi kutuluka panja, ndipo anapita kumalo kopanda anthu.+ Kumeneko anayamba kupemphera.+