Salimo 55:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Usiku, m’mawa ndi masana ndimakhala ndi nkhawa ndipo ndimakhala ndikulira,+Choncho Mulungu amamva mawu anga.+ Salimo 119:147 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 147 Ndadzuka m’mawa kuli mbuu,+ kuti ndipemphe thandizo kwa inu,+Pakuti ndayembekezera mawu anu.+
17 Usiku, m’mawa ndi masana ndimakhala ndi nkhawa ndipo ndimakhala ndikulira,+Choncho Mulungu amamva mawu anga.+