Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 88:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 88 Inu Yehova, Mulungu wa chipulumutso changa,+

      Masana ndimafuula kwa inu,+

      Usikunso ndimafuula pamaso panu.+

  • Salimo 119:147
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 147 Ndadzuka m’mawa kuli mbuu,+ kuti ndipemphe thandizo kwa inu,+

      Pakuti ndayembekezera mawu anu.+

  • Danieli 6:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Koma Danieli atangodziwa kuti lamulo limeneli lasainidwa, analowa m’nyumba mwake, ndipo mawindo a nyumba yake oyang’ana ku Yerusalemu+ anali otsegula. M’nyumbamo, iye anali kugwada ndi kupemphera+ kwa Mulungu wake ndi kumutamanda+ katatu pa tsiku,+ monga mmene anali kuchitira nthawi zonse lamuloli lisanasainidwe.+

  • Maliko 1:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 M’mawa kwambiri kukali mdima, Yesu anadzuka ndi kutuluka panja, ndipo anapita kumalo kopanda anthu.+ Kumeneko anayamba kupemphera.+

  • 1 Atesalonika 5:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Muzipemphera mosalekeza.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena