Luka 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno Yesu anawauza fanizo pofuna kuwasonyeza kufunika koti azipemphera nthawi zonse, osaleka.+ Aroma 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kondwerani ndi chiyembekezocho.+ Pirirani chisautso.+ Limbikirani kupemphera.+