Salimo 88:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 88 Inu Yehova, Mulungu amene amandipulumutsa,+Masana ndimafuulira inu,Ndipo usiku ndimabwera pamaso panu.+
88 Inu Yehova, Mulungu amene amandipulumutsa,+Masana ndimafuulira inu,Ndipo usiku ndimabwera pamaso panu.+