Salimo 27:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Musandibisire nkhope yanu.+ Musabweze mtumiki wanu mutakwiya. Inu ndi amene mumandithandiza.+Musanditaye kapena kundisiya, inu Mulungu amene mumandipulumutsa. Yesaya 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Taonani! Mulungu ndi chipulumutso changa.+ Ndidzamukhulupirira ndipo sindidzaopa chilichonse,+Chifukwa Ya,* Yehova, ndi mphamvu zanga komanso nyonga zanga,Ndipo iye wakhala chipulumutso changa.”+
9 Musandibisire nkhope yanu.+ Musabweze mtumiki wanu mutakwiya. Inu ndi amene mumandithandiza.+Musanditaye kapena kundisiya, inu Mulungu amene mumandipulumutsa.
2 Taonani! Mulungu ndi chipulumutso changa.+ Ndidzamukhulupirira ndipo sindidzaopa chilichonse,+Chifukwa Ya,* Yehova, ndi mphamvu zanga komanso nyonga zanga,Ndipo iye wakhala chipulumutso changa.”+