Salimo 27:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Musandibisire nkhope yanu.+Musabweze mtumiki wanu mutakwiya.+Inu mukhale mthandizi wanga.+Musanditaye ndi kundisiya, inu Mulungu wa chipulumutso changa.+
9 Musandibisire nkhope yanu.+Musabweze mtumiki wanu mutakwiya.+Inu mukhale mthandizi wanga.+Musanditaye ndi kundisiya, inu Mulungu wa chipulumutso changa.+