1 Samueli 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako Samueli anatenga mwala+ ndi kuuimika pakati pa Mizipa ndi Yesana ndipo anautcha dzina lakuti Ebenezeri,* n’kunena kuti: “Lero Yehova watithandiza ngati kale.”+ Salimo 46:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Mulungu ndiye pothawira pathu ndi mphamvu yathu,+Thandizo lopezeka mosavuta pa nthawi ya masautso.+
12 Kenako Samueli anatenga mwala+ ndi kuuimika pakati pa Mizipa ndi Yesana ndipo anautcha dzina lakuti Ebenezeri,* n’kunena kuti: “Lero Yehova watithandiza ngati kale.”+
46 Mulungu ndiye pothawira pathu ndi mphamvu yathu,+Thandizo lopezeka mosavuta pa nthawi ya masautso.+