9 Panalinso miyala ina 12 imene Yoswa anaisanjikiza pakati pa mtsinje wa Yorodano, pamalo amene anaimapo+ ansembe onyamula likasa la pangano. Miyalayo ilipo mpaka lero.
26 Ndiyeno Yoswa analemba mawu amenewa m’buku la chilamulo cha Mulungu.+ Atatero, anatenga mwala waukulu+ ndi kuuika pansi pa mtengo waukulu kwambiri+ umene uli pafupi ndi malo opatulika a Yehova.