Salimo 88:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 88 Inu Yehova, Mulungu wa chipulumutso changa,+Masana ndimafuula kwa inu,+Usikunso ndimafuula pamaso panu.+
88 Inu Yehova, Mulungu wa chipulumutso changa,+Masana ndimafuula kwa inu,+Usikunso ndimafuula pamaso panu.+