Salimo 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inu Yehova, m’mawa mudzamva mawu anga,+M’mawa ndidzalankhula nanu ndipo ndidzadikira yankho.+ Salimo 46:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Mulungu ndiye pothawira pathu ndi mphamvu yathu,+Thandizo lopezeka mosavuta pa nthawi ya masautso.+
46 Mulungu ndiye pothawira pathu ndi mphamvu yathu,+Thandizo lopezeka mosavuta pa nthawi ya masautso.+