Salimo 55:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Usiku, m’mawa ndi masana ndimakhala ndi nkhawa ndipo ndimakhala ndikulira,+Choncho Mulungu amamva mawu anga.+ Salimo 88:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma ine ndafuulira inu Yehova kupempha thandizo,+Ndipo m’mawa mapemphero anga amafika kwa inu nthawi zonse.+
17 Usiku, m’mawa ndi masana ndimakhala ndi nkhawa ndipo ndimakhala ndikulira,+Choncho Mulungu amamva mawu anga.+
13 Koma ine ndafuulira inu Yehova kupempha thandizo,+Ndipo m’mawa mapemphero anga amafika kwa inu nthawi zonse.+