Maliko 1:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 M’mawa kwambiri kukali mdima, Yesu anadzuka ndi kutuluka panja, ndipo anapita kumalo kopanda anthu.+ Kumeneko anayamba kupemphera.+
35 M’mawa kwambiri kukali mdima, Yesu anadzuka ndi kutuluka panja, ndipo anapita kumalo kopanda anthu.+ Kumeneko anayamba kupemphera.+