Mateyu 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma poyankha iye anati: “Malemba amati, ‘Munthu sangakhale ndi moyo ndi chakudya chokha, koma ndi mawu onse otuluka pakamwa pa Yehova.’”*+ Mateyu 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma akakuperekani kumeneko, musade nkhawa za mmene mukalankhulire kapena zimene mukanene. Mudzapatsidwa nthawi yomweyo zoti mulankhule,+
4 Koma poyankha iye anati: “Malemba amati, ‘Munthu sangakhale ndi moyo ndi chakudya chokha, koma ndi mawu onse otuluka pakamwa pa Yehova.’”*+
19 Koma akakuperekani kumeneko, musade nkhawa za mmene mukalankhulire kapena zimene mukanene. Mudzapatsidwa nthawi yomweyo zoti mulankhule,+