Mateyu 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma akadzakupititsani kumeneko, musadzade nkhawa kuti mudzalankhula bwanji kapena kuti mudzanena chiyani, chifukwa zoti mulankhule mudzapatsidwa nthawi yomweyo.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:19 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),9/2021, ptsa. 24-25
19 Koma akadzakupititsani kumeneko, musadzade nkhawa kuti mudzalankhula bwanji kapena kuti mudzanena chiyani, chifukwa zoti mulankhule mudzapatsidwa nthawi yomweyo.+