Salimo 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndichitireni zimenezi kuti ndilengeze ntchito zanu zonse zotamandika+Pazipata+ za mwana wamkazi wa Ziyoni,+Kuti ndikondwere ndi chipulumutso chanu.+ Salimo 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma ine ndakhulupirira kukoma mtima kwanu kosatha.+Mtima wanga ukondwere chifukwa cha chipulumutso chanu.+
14 Ndichitireni zimenezi kuti ndilengeze ntchito zanu zonse zotamandika+Pazipata+ za mwana wamkazi wa Ziyoni,+Kuti ndikondwere ndi chipulumutso chanu.+
5 Koma ine ndakhulupirira kukoma mtima kwanu kosatha.+Mtima wanga ukondwere chifukwa cha chipulumutso chanu.+