Salimo 40:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Onse amene akufunafuna inu,+Akondwere ndi kusangalala mwa inu.+Onse amene amakonda chipulumutso chanu,+Nthawi zonse azinena kuti: “Yehova alemekezeke.”+
16 Onse amene akufunafuna inu,+Akondwere ndi kusangalala mwa inu.+Onse amene amakonda chipulumutso chanu,+Nthawi zonse azinena kuti: “Yehova alemekezeke.”+