Deuteronomo 4:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Mukadzafufuza Yehova Mulungu wanu muli kumeneko, mudzam’pezadi,+ chifukwa mudzam’funafuna ndi mtima wanu wonse ndiponso moyo wanu wonse.+ Salimo 70:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Onse amene akufunafuna inu akondwere ndi kusangalala mwa inu,+Ndipo onse amene amakonda chipulumutso chanu, nthawi zonse azinena kuti: “Mulungu alemekezeke!”+
29 “Mukadzafufuza Yehova Mulungu wanu muli kumeneko, mudzam’pezadi,+ chifukwa mudzam’funafuna ndi mtima wanu wonse ndiponso moyo wanu wonse.+
4 Onse amene akufunafuna inu akondwere ndi kusangalala mwa inu,+Ndipo onse amene amakonda chipulumutso chanu, nthawi zonse azinena kuti: “Mulungu alemekezeke!”+