Salimo 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma onse othawira kwa inu adzakondwa.+Adzafuula mokondwera mpaka kalekale.*+Ndipo inu mudzawateteza.Okonda dzina lanu adzakondwa chifukwa cha inu.+ Maliro 3:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Yehova ndi wabwino kwa munthu amene akumuyembekezera,+ kwa munthu amene akumufunafuna.+
11 Koma onse othawira kwa inu adzakondwa.+Adzafuula mokondwera mpaka kalekale.*+Ndipo inu mudzawateteza.Okonda dzina lanu adzakondwa chifukwa cha inu.+