Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 30:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 moti mwabwerera kwa Yehova Mulungu wanu+ ndi kumvera mawu ake ndi mtima wanu wonse ndi moyo wanu wonse,+ mogwirizana ndi zonse zimene ndikukulamulani lero, inuyo ndi ana anu,

  • 1 Mafumu 8:48
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 48 n’kubwerera kwa inu ndi mtima wawo wonse+ ndi moyo wawo wonse, m’dziko la adani awo amene anawagwira ndiponso akapemphera kwa inu atayang’ana kudziko lawo limene munapatsa makolo awo, kumzinda umene mwasankha ndi nyumba ya dzina lanu imene ndamanga,+

  • Yeremiya 29:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 “‘Inu mudzandifunafuna ndipo mudzandipeza+ chifukwa mudzandifunafuna ndi mtima wanu wonse.+

  • Yoweli 2:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Yehova wanenanso kuti, “Tsopano bwererani kwa ine ndi mtima wanu wonse.+ Salani kudya,+ lirani momvetsa chisoni ndiponso mokuwa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena