Deuteronomo 29:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Choncho muzisunga mawu a pangano ili kuti zonse zimene muzichita zizikuyenderani bwino.+ Yoswa 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Buku la malamulo ili lisachoke pakamwa pako,+ uziliwerenga ndi kusinkhasinkha usana ndi usiku, kuti uonetsetse kuti ukutsatira zonse zolembedwamo.+ Pakuti ukatero, udzakhala ndi moyo wopambana, ndipo udzachita zinthu mwanzeru.+
8 Buku la malamulo ili lisachoke pakamwa pako,+ uziliwerenga ndi kusinkhasinkha usana ndi usiku, kuti uonetsetse kuti ukutsatira zonse zolembedwamo.+ Pakuti ukatero, udzakhala ndi moyo wopambana, ndipo udzachita zinthu mwanzeru.+